Home 2

Mkulu owona mapulani a za chitukuko ku Mangochi a Chris Nawata ati nkhani yosamba m’manja yatsamira pakusintha kaganizidwe ndipo khonsoloyi ikudalira adindo ngati mafumu, atsogoleri a mabungwe komanso zipembedzo …