Bungwe la MEJN la chilimika pa ntchito yolimbikitsa maganizo am’gwiro pakati pa achinyamata m’boma la Mangochi.
Bungwe la Malawi Economic Justice Network MEJN lati ndi lodzipereka pa ntchito yolimbikitsa maganizo am’gwiro (Mental Health pachingerezi) pakati pa achinyamata m’dera…