Dodma ili tcheru ngati madzi angasefukire
Nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzi ya Department of Disaster Management Affairs- Dodma yati ili tcheru powonetsetsa kuti katundu ndi miyoyo ya…
Nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzi ya Department of Disaster Management Affairs- Dodma yati ili tcheru powonetsetsa kuti katundu ndi miyoyo ya…
Bungwe la Malawi Economic Justice Network MEJN lati ndi lodzipereka pa ntchito yolimbikitsa maganizo am’gwiro (Mental Health pachingerezi) pakati pa achinyamata m’dera…
Ntchito za Climate Just Communities, akuti zayenda bwino ndipo zipindulira anthu a m’maboma okwana 7 omwe ntchitozi zimagwilidwa.Polankhula pa mkumano wa mabungwe…
Mkulu owona mapulani a za chitukuko ku Mangochi a Chris Nawata ati nkhani yosamba m’manja yatsamira pakusintha kaganizidwe ndipo khonsoloyi ikudalira adindo…
M’khala kale pa ndale a Patricia Kaliati achenjeza amayi omwe akupikisana nawo pa chisankho cha sabata la mawa kuti achepetse kudziyenereza kuti…
A 60-year-old man has tragically died after being attacked by a wild elephant in Namizimu Forest Reserve, near Kwilasya Village under Traditional…
Ogwira ntchito kumsika wa Monkey-Bay omwe ndi alonda komanso otolera misonkho omwe amagwira ntchito pansi pa Khonsolo ya boma la Mangochi adandaula…
Anthu ochuluka lero, 2 April 2025, mamawa anakhamukira ku msika wa Sumbi ku Monkey Bay m’boma la Mangochi komwe amakaona mnyamata wina…
Bwalo loweruza milandu la Mangochi First Grade Magistrate lapeza a Steven Ajasi a zaka 45 olakwa ndikuwalipiritsa chindapusa cha ndalama zokwana K800,…
M’modzi mwa achinyamata oyimba Chamba cha Afro Hip-Hop Ku Monkey Bay m’boma la Mangochi yemwe amadziwika ndi dzina la “SHYZEE” wamwalira m’bandakucha…