Moyo ukulimba: Malipiro sakuoneka
Ogwira ntchito kumsika wa Monkey-Bay omwe ndi alonda komanso otolera misonkho omwe amagwira ntchito pansi pa Khonsolo ya boma la Mangochi adandaula…
Ogwira ntchito kumsika wa Monkey-Bay omwe ndi alonda komanso otolera misonkho omwe amagwira ntchito pansi pa Khonsolo ya boma la Mangochi adandaula…
Bwalo loweruza milandu la Mangochi First Grade Magistrate lapeza a Steven Ajasi a zaka 45 olakwa ndikuwalipiritsa chindapusa cha ndalama zokwana K800,…
Ngati njira imodzi yofuna kuchepetsa ngozi mu nseu wa Mangochi-Monkey-bay, phungu wa dera la Monkey bay, a Ralph Jooma ayamba ntchito yokonza…